eBook INGLÉS EPUB sin DRM

Zinsinsi za Chikhulupiriro

Por DAG HEWARD-MILLS

Léelo en cualquier dispositivo Descárgalo y empieza a leer ya







Sinopsis

Phunziro losangalatsa komanso lozama ili pa mutu wa "chikhulupiriro" lidzakopa wina aliyense yemwe cholinga chake ndi kukondweretsa Mulungu. Pakuti popanda chikhulupiriro nzosatheka kukondweretsa Mulungu, malemba amanena choncho.

Ichi ndichifukwa chake bukuli ndilofunika kuwerengedwa ndi aliyense amene ali ndi chikhumbo chokondweretsa Mulungu. Ngati chikhulupiriro chinapangitsa Abrahamu kukhala bwenzi la Mulungu, ndiye kuti chikhulupiriro nchofunika kwambiri pa kuyenda kwathu ndi Mulungu. Bukuli ndi chuma chenicheni! Dziwani zinsinsi zofunika kuti muyende ndi kukhala ndi moyo mwa chikhulupiriro. Tsegulani zinsinsi za chikhulupiriro zomwe mukuzifunikira kuti muchite zinthu zosatheka mmoyo wanu!

Novedades que no querrás perderte

Ver más

Léelo en cualquier dispositivo


Ficha Técnica

Editorial: Dag Heward-mills

ISBN: 9798224655816

Idioma: Inglés

Fecha de lanzamiento: 28/12/2025

Especificaciones del producto

Reseñas sobre Zinsinsi za Chikhulupiriro

Comparte tu experiencia con la comunidad lectora.

0

0 Reseñas

5 0
4 0
3 0
2 0
1 0

Sólo por opinar entras en el sorteo mensual de tres tarjetas regalo valoradas en
20€

Los eBooks más vendidos de la semana

Ver más